Mawu Amunsi
a Timayamikila kwambili kuti Yehova anatipatsa mwayi wopemphela kwa iye. Timafuna kuti mapemphelo athu azikhala ngati zofukiza za fungo lokoma, kuti iye azikondwela nawo. M’nkhani ino, tikambilane zimene tingachule m’mapemphelo athu. Tikambilanenso mfundo zofunika kukumbukila tikapatsidwa mwayi woimilako ena m’pemphelo.