Mawu Amunsi
b Tikadziŵa kuti wina mu mpingo wacita chimo lalikulu, tiyenela kumuuza kuti akauze akulu nkhaniyo. Ngati iye sakucita zimenezo, kukhulupilika kwathu kwa Yehova komanso ku mpingo wacikhristu, kudzatipangitsa kukawauza abusa auzimu za chimo lakelo.