Mawu Amunsi
a Nkhani ino, ifotokoza kusintha kwa kamvedwe kathu pa mawu a Yesu a pa Yohane 5:28, 29 akuti anthu “adzauka kuti alandile moyo,” komanso akuti “adzauka kuti aweluzidwe.” Tikambilane zimene ciukitso ca magulu aŵili amenewa cimatanthauza, komanso anthu amene ali m’magulu amenewa.