Mawu Amunsi
b Bukuli linayamba kulembedwa “kucokela pa kukhazikitsidwa kwa dziko.” Mawu akuti dziko pa lembali, akutanthauza anthu amene ali na mwayi woomboledwa ku uchimo. (Mat. 25:34; Chiv. 17:8) Mwacidziŵikile, munthu wolungama Abele, ndiye woyamba kulembedwa dzina m’buku la moyo limeneli.