Mawu Amunsi
a Nkhani ino ifotokoza kusintha kwa kamvedwe kathu ponena za nchito yaikulu yophunzitsa anthu yochulidwa pa Danieli 12:2, 3. Tikambilane kuti nchito imeneyi idzacitika liti, komanso amene akuloŵetsedwamo. Tionenso mmene nchito yophunzitsa imeneyo idzathandizila anthu padziko lapansi kukonzekela mayeso othela kumapeto kwa Ulamulilo wa Khristu wa Zaka Cikwi.