Mawu Amunsi
d Komabe, mawu akuti “olungama” komanso “osalungama” opezeka pa Machitidwe 24:15, komanso mawu akuti “amene anali kucita zabwino” ndiponso akuti “amene anali kucita zoipa” a pa Yohane 5:29, kwenikweni amanena za nchito zimene oukitsidwawo anacita asanafe.