Mawu Amunsi
b Pali zifukwa zitatu zimene ziyenela kuti zinapangitsa Danieli kukana kudya cakudya ca Ababulo: (1) Nyama zimene Ababulo anali kudya zinali zoletsedwa m’Cilamulo. (Deut. 14:7, 8) (2) N’kutheka kuti nyama zimenezo zinali zosakhetsa. (Lev. 17:10-12) (3) Kudya nyamazo kukanakhala ngati kulambila milungu yonyenga.—Yelekezelani na Levitiko 7:15 komanso 1 Akorinto 10:18, 21, 22.