Mawu Amunsi
d Mungapeze mfundo zothandiza pa jw.org na m’zofalitsa zathu. Mwacitsanzo, onani nkhani yakuti, “Pornography Can Shatter Your Marriage” pa jw.org; “Mungathe Kukana Mayesero!” mu Nsanja ya Mlonda ya, April 1, 2014, masa. 10-12; komanso yakuti “Kodi Zamalisece Zilibe Vuto?” mu Nsanja ya Mlonda ya, August 1, 2013, masa. 3-7.