Mawu Amunsi a Poyamba, mau a pa Ezara 4:8-6:18, 7:12-26; Yeremiya 10:11, ndi pa Danieli 2:4b-7:28 analembedwa m’Ciaramu.