Mawu Amunsi
b Liu lakuti Septuagint limatanthauza “70.” Zioneka kuti nchito yomasulila malembawa inayamba zaka pafupifupi 300 Kristu asanabadwe ndipo inatha pambuyo pa zaka 150. Baibulo la Septuagint likali lofunika masiku ano cifukwa limathandiza akatswili kumvetsa mau ndi mavesi ovuta aciheberi.