Mawu Amunsi
b Buku lakuti New Catholic Encyclopedia, Gawo Laciŵili, voliyumu 14, masamba 883-884, imati: “Pambuyo pomasulidwa ku ukapolo, dzina lakuti Yahweh inayamba kuonedwa kukhala yapadela kwambili, ndipo anayamba kuiseŵenzetsa kwambili m’malo mwa mawu akuti ADONAI kapena ELOHIM.”