Mawu Amunsi
a Baibo limaseŵenzetsa liwu lakuti “mtundu” limene limatanthauza zambili kuposa liwu lacingelezi lakuti “species” limene asayansi amasewenzetsa. Kambili zimene asayansi amati ni kusandulika kukhala mtundu watsopano zimangokhala kusiyanako cabe kwa zamoyo za mtundu umodzi, monga mmene liwuli analisewenzetsela mu buku la Genesis.