October Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano October 2017 Maulaliki a Citsanzo October 2-8 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | DANIELI 7-9 Ulosi wa Danieli Unakambilatu za Kubwela kwa Mesiya UMOYO WATHU WACIKHRISTU Khalani Woŵelenga Malemba Wakhama October 9-15 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | DANIELI 10-12 Yehova Anaonelatu Tsogolo la Mafumu October 16-22 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | HOSEYA 1-7 Cikondi Cokhulupilika Cimam’kondweletsa Yehova—Nanga Imwe? October 23-29 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | HOSEYA 8-14 M’patseni Zabwino Koposa Yehova UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kukhala na Umoyo Wotamanda Yehova October 30–November 5 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOWELI 1-3 “Ana Anu Aamuna ndi Ana Anu Aakazi Adzanenela”