November Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, November-December 2022 November 7-13 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Ife Tili ndi Ambili Kuposa Amene Ali ndi Iwo UMOYO WATHU WACIKHRISTU “Khalani Opatsa” November 14-20 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anapangitsa Zinthu Zosayembekezeleka Kucitika November 21-27 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Anacita Zinthu Molimba Mtima, Modzipeleka, Komanso Mokangalika UMOYO WATHU WACIKHRISTU Zimene Zingakuthandizeni Kupewa Kuzengeleza November 28–December 4 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mayi Woipa Komanso Wofunitsitsa Ulamulilo Analangidwa CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Nyumba Yonse ya Ahabu Idzafafanizidwa”—2 Maf. 9:8 UMOYO WATHU WACIKHRISTU “N’cifukwa Ciyani Akhristu Ayenela Kuyesetsa Kuwonjezela Utumiki Wawo?” December 5-11 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kucita Zinthu na Mtima Wonse Kumabweletsa Madalitso Oculuka UMOYO WATHU WACIKHRISTU Yehova Saiŵala Nchito Yathu Imene Timagwila Molimbika December 12-18 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli na Malile UMOYO WATHU WACIKHRISTU Muziyembekezela Mapeto a Dzikoli Mopanda Mantha December 19-25 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Adani Athu Amacita Poyesa Kutifooketsa UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kondwelani Pamene Mukuzunzidwa December 26–January 1 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Pemphelo Linasonkhezela Yehova Kucitapo Kanthu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Mapemphelo Athu ni Amtengo Wapatali kwa Yehova CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo