LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 7
  • Yesu Anali Kutsitsimula Anthu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yesu Anali Kutsitsimula Anthu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • “Bwelani kwa Ine . . . Ndipo Ndidzakutsitsimutsani”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Kukoma Mtima Ndi Khalidwe Lofunika Kwambiri
    Imbirani Yehova
  • Mphamvu ya Kukoma Mtima
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 10-11

Yesu Anali Kutsitsimula Anthu

11:28-30

Mkazi wa m’nthawi ya Baibo wanyamula goli

“Goli Langa ndi Lofewa”

Popeza kuti Yesu anali kalipentala, anali kudziŵa mopangila goli, mwina kulikulunga na nsalu kapena cikumba kuti lisamapweteke. Pamene tinyamula goli lokhala wophunzila wa Yesu pa ubatizo wathu, timayamba kugwila nchito yovuta, ndi kulandila maudindo. Ngakhale n’conco, kucita zimenezi n’kotsitsimula ndipo kumabweletsa madalitso.

Kodi mwapeza madalitso anji kucokela pamene munanyamula goli la Yesu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani