LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 2
  • April 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 2

April 2-8

MATEYU 26

  • Nyimbo 19 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Pasika na Cikumbutso—Kulingana na Kusiyana Kwake”: (10 min.)

    • Mat. 26:17-20—Yesu anadya Pasika yotsiliza na atumwi ake (“Cakudya ca pa Pasika” nwtsty zithunzi)

    • Mat. 26:26—Mkate wa pa Cikumbutso umaimila thupi la Yesu (“ukuimila” nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 26:27, 28—Vinyo wa pa Cikumbutso umaimila ‘magazi a pangano’ a Yesu (“magazi a pangano” nwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 26:17—N’cifukwa ciani tingakambe kuti Nisani 13 ni “tsiku loyamba la cikondwelelo ca mikate yopanda cofufumitsa”? (“Pa tsiku loyamba la cikondwelelo ca mikate yopanda cofufumitsa” nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 26:39—N’ciani ciyenela kuti cinasonkhezela Yesu kupemphela kuti: “kapu iyi indipitilile”? (“kapu iyi indipitilile” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 26:1-19

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 59 pala. 21-22 na zakumapeto

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 20

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.)

  • Khala Bwenzi la Yehova—Dipo: (7 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Pambuyo pake, itanani ana amene munasankha kuti abwele ku pulatifomu, na kuwafunsa mafunso aya: N’cifukwa ciani anthu amadwala, kukalamba, na kufa? Kodi Yehova watipatsa ciyembekezo canji? Kodi iwe ufuna ukaonane na ndani m’paradaiso?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 15

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 74 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani