-
Kodi Baibo Imati Ciyani pa Nkhani ya Umbeta na Ukwati?Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
-
-
7. Sungani malamulo a Yehova mu ukwati wanu
Pafunikila khama kuti munthu azitsatila malamulo a Yehova mu ukwati.c Ndipo Yehova amadalitsa amene amayesetsa kutelo. Tambani VIDIYO.
Ŵelengani Aheberi 13:4, na kukambilana mafunso aya:
Kodi muganiza n’zotheka kutsatila malamulo a Yehova a mu ukwati? Mwayankha conco cifukwa ciyani?
Yehova amafuna kuti Akhristu akakwatilana kapena kusudzulana azilembetsa ku boma. M’maiko ambili, izi n’zimene malamulo amafuna. Ŵelengani Tito 3:1, na kukambilana funso ili:
Ngati muli pabanja, kodi mukutsimikiza kuti ukwati wanu ni wolembetsa ku boma?
-
-
Kodi Baibo Imati Ciyani pa Nkhani ya Umbeta na Ukwati?Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
-
-
c Ngati munangotengana cabe na munthu amene simunamange naye ukwati, muyenela kupanga cisankho inu mwini, cokamangitsa naye ukwati kapena kusiyana naye.
-