LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 44
  • Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Timasangalala Kuthandizila pa Nchito Yokolola
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Tikhala Monga mwa Dzina Lathu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Zochita Zathu Zizigwirizana ndi Dzina Lathu
    Imbirani Yehova
  • Zotsatilapo za Nchito Yolalikila—“M’mindamo, Mwayela Kale Ndipo m’Mofunika Kukolola”
    Ufumu wa Mulungu Ukulamulila
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 44

Nyimbo 44

Tigwire Ntchito Yokolola Mosangalala

(Mateyo 13:1-23)

1. Tili munthawi yokolola,

Ndi mwayitu wapadera.

Okololawo ndi angelo

Nafe tikolole nawo.

Yesu watipatsa chitsanzo

Potitsogolera m’munda.

Ndi mwayidi womwe tapatsidwa

Kuchita nawo ntchitoyi.

2. Tikugwira nawo ntchitoyi

Pokonda M’lungu ndi m’nansi.

Ulaliki ndi kukolola

Zonse zili zofunika,

Ndife osangalala zedi

Pogwira ntchito ndi M’lungu.

Choncho tipirire pantchitoyi

M’lungu adzatidalitsa.

(Onaninso Mat. 24:13; 1 Akor. 3:9; 2 Tim. 4:2.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani