LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 31
  • Uziyenda na Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Uziyenda na Mulungu
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Yendani ndi Mulungu!
    Imbirani Yehova
  • “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti”
    Imbirani Yehova
  • ‘Tsimikizilani Zinthu Zofunika Kwambili’
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Kuyenda ndi Yehova Tsiku na Tsiku
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 31

NYIMBO 31

Uziyenda na Mulungu

Yopulinta

(Mika 6:8)

  1. 1. Uziyenda na Mulungu;

    Khala wodzicepetsa.

    Umudalile, muyandikile.

    Adzakulimbikitsa.

    Ukaphunzila coonadi,

    Siudzapatuka.

    Gwila dzanja la Mulungu,

    Adzakutsogolela.

  2. 2. Uziyenda na Mulungu;

    Pewa zinthu zoipa.

    Olo ziyeso zikule bwanji,

    Iwe udzapambana.

    Zinthu zonse zotamandika

    Uziganizile.

    Ukadalila Yehova,

    Udzakhala wolimba.

  3. 3. Ukayenda na Mulungu;

    Udzapeza cimwemwe.

    Udzakondwela kuti Yehova

    Lomba ni bwenzi lako.

    Ngati uyenda na Mulungu

    Adzakudalitsa.

    Khala ku mbali ya M’lungu

    Kuti udalitsidwe.

(Onaninso Gen. 5:24; 6:9; Afi. 4:8; 1 Tim. 6:6-8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani