LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 134
  • Ana ni Mphatso Zimene Mulungu Amaikiza kwa Makolo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ana ni Mphatso Zimene Mulungu Amaikiza kwa Makolo
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Ana Ndi Mphatso Yochokera kwa Mulungu
    Imbirani Yehova
  • N’zotheka Kuti Muziwadalila Abale Anu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Abusa ni Mphatso za Amuna
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Munapeleka Mwana Wanu Wokondeka
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 134

NYIMBO 134

Ana ni Mphatso Zimene Mulungu Amaikiza kwa Makolo

Yopulinta

(Salimo 127:3-5)

  1. 1. Mwamuna na mkazi wake,

    Ngati iwo akhala na mwana,

    Afunika akumbukile

    Mwanayo si wawo okha.

    Mphatso yocokela kwa M’lungu,

    Iye ndiye anapanga zonse.

    Kwa makolo amapeleka

    Malangizo oŵathandiza.

    (KOLASI)

    Mphatso iyi ni yapadela,

    Inu muisamalile.

    Mwana wanu mumuthandize

    Aphunzile coonadi.

  2. 2. Malamulo a Yehova

    Muziwasunga mumtima mwanu.

    Muziphunzitsa ana anu;

    Uwu ni udindo wanu.

    Muziŵaphunzitsa poyenda,

    Pouka na panthawi yopuma.

    Ndipo iwo sadzaiŵala.

    Yehova adzaŵadalitsa.

    (KOLASI)

    Mphatso iyi ni yapadela,

    Inu muisamalile.

    Mwana wanu mumuthandize

    Aphunzile coonadi.

(Onaninso Deut. 6:6, 7; Aef. 6:4; 1 Tim. 4:16.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani