LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 July tsa. 5
  • Kodi Zolengedwa Zimatiphunzitsa Ciani za Kulimba Mtima?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Zolengedwa Zimatiphunzitsa Ciani za Kulimba Mtima?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • ‘Limba Mtima, Ugwile Nchito Mwamphamvu’
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nilimbitseni Mtima
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Kulitsani Makhalidwe Aumulungu—Kulimba Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 July tsa. 5
Tate na mwana wake aimilila m’mbali mwa nyanja akuyang’ana mapili capatali.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kodi Zolengedwa Zimatiphunzitsa Ciani za Kulimba Mtima?

Yehova amatiphunzitsa mmene tingaonetsele makhalidwe aumulungu. Iye amacita izi kupitila mu zitsanzo za amuna na akazi ochulidwa m’Baibo. Komabe, zolengedwa zake nazonso zimatiphunzitsa mfundo zofunika. (Yobu 12:7, 8) Kodi tingaphunzile ciani za kulimba mtima kwa mkango, hosi, mshulu, cozo, komanso njovu?

TAMBITSANI VIDIYO YAKUTI TIPHUNZILE KULIMBA MTIMA KU ZOLENGEDWA, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO OTSATILAWA:

  • Mkango waukazi ukumwa madzi pamodzi na ana ake.

    Kodi mikango yaikazi imaonetsa bwanji kulimba mtima pamene iteteza ana awo?

  • Mahosi akuthamanga mthengo.

    Kodi mahosi amaphunzitsidwa bwanji kukhala olimba mtima pa nkhondo?

  • Kamshulu kakumenyana na njoka.

    N’cifukwa ciani mshulu suopa njoka zapoizoni?

  • Cozo akuteteza malo ake kuli cozo mnzake.

    Kodi cozo amaonetsa bwanji kulimba mtima?

  • Gulu la njovu ikuyenda.

    Kodi njovu zimathandizana bwanji molimba mtima poteteza njovu zina m’gulu lawo?

  • Kodi nyama zimenezi zitiphunzitsa ciani za kulimba mtima?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani