LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 126
  • Khalani Maso, Cilimikani, Khalani Amphamvu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalani Maso, Cilimikani, Khalani Amphamvu
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Khalani Maso, Limbani, Khalani Amphamvu
    Imbirani Yehova
  • Thawirani ku Ufumu wa Mulungu
    Imbirani Yehova
  • Adzakulimbitsa
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mulungu Adzakupatsani Mphamvu
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 126

NYIMBO 126

Khalani Maso, Cilimikani, Khalani Amphamvu

Yopulinta

(1 Akorinto 16:13)

  1. 1. Khalani ocilimika,

    Ndipo khalani maso.

    Mukhale olimba mtima,

    Inu mudzapambana.

    Timvela lamulo la Yesu;

    Timaima ku mbali yake.

    (KOLASI)

    Tiyeni’fe tikhale maso

    Mpaka cabe mapeto!

  2. 2. Tetezani maganizo,

    Khalanibe omvela.

    Tsatilani malangizo

    A Yesu Khristu Mfumu.

    Mvelani akulu mu mpingo

    Amene amatiteteza.

    (KOLASI)

    Tiyeni’fe tikhale maso

    Mpaka cabe mapeto!

  3. 3. Tikhale ogalamuka,

    Ndipo tigwilizane.

    Olo adani atsutse

    Tidzalalikilabe.

    Timutamande M’lungu wathu;

    Tsiku lake layandikila.

    (KOLASI)

    Tiyeni’fe tikhale maso

    Mpaka cabe mapeto!

(Onaninso Mat. 24:13; Aheb. 13:7, 17; 1 Pet. 5:8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani