LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 16
  • Tamandani Ya Kaamba ka Mwana Wake Wodzozedwayo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tamandani Ya Kaamba ka Mwana Wake Wodzozedwayo
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tamandani Yehova Chifukwa cha Ufumu Wake
    Imbirani Yehova
  • Tiyeni Tonse Titamande Ya
    Imbirani Yehova
  • Tamandani Yehova
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Tipita Nanu Limodzi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 16

NYIMBO 16

Tamandani Ya Kaamba ka Mwana Wake Wodzozedwayo

Yopulinta

(Chivumbulutso 21:2)

  1. 1. Yehova ‘nasankha Yesu

    Kuti alamulile.

    Afuna cifunilo cake

    Padzikoli cicitike.

    (KOLASI)

    Tamandani Yehova M’lungu

    Iye anasankha Yesu.

    Tsopano Khristu wakhala Mfumu

    ya Ufumu wa M’lungu.

    Tamandani Yehova M’lungu,

    Tamandani Yesu Khristu.

    Adzayeletsa dzina loyela

    la Atate Yehova.

  2. 2. Abale a Yesu Khristu

    Nawo anasankhiwa.

    Capamodzi na Yesu Mfumu

    Adzalamulila konse.

    (KOLASI)

    Tamandani Yehova M’lungu

    Iye anasankha Yesu.

    Tsopano Khristu wakhala Mfumu

    ya Ufumu wa M’lungu.

    Tamandani Yehova M’lungu,

    Tamandani Yesu Khristu.

    Adzayeletsa dzina loyela

    la Atate Yehova.

(Onaninso Miy. 29:4; Yes. 66:7, 8; Yoh. 10:4; Chiv. 5:9, 10.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani