LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • ll gao 6 masa. 14-15
  • Kodi Cigumula ca Nowa Cimatiphunzitsa Ciani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Cigumula ca Nowa Cimatiphunzitsa Ciani?
  • Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Nkhani Zofanana
  • Gao 6
    Mvetselani kwa Mulungu
  • Kutengapo Phunzilo pa Zimene Zinacitika Kumbuyo
    Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu!
  • Cigumula ca Nowa—Ndani Anamvetsela? Ndani Sanamvetsele?
    Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Anam’sunga “Pomupulumutsa Pamodzi ndi Anthu Ena 7”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
Onaninso Zina
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
ll gao 6 masa. 14-15

GAO 6

Kodi Cigumula ca Nowa Cimatiphunzitsa Ciani?

Mulungu anaononga anthu oipa koma anapulumutsa Nowa ndi banja lake. Genesis 7:11, 12, 23

Cingalawa cili pamwamba pa madzi, anthu oipa akumila m’madzi, ndipo angelo oipa avula matupi aumunthu

Kunagwa mvula masiku 40 usana ndi usiku, ndipo dziko lonse lapansi linamila. Anthu onse oipa anafa.

Angelo opanduka anasiya matupi awo aumunthu ndi kukhala viŵanda.

Zinyama komanso Nowa na banja lake atuluka m’cingalawa, ndipo utawaleza uonekela kumwamba

Anthu amene anali m’cingalawa anapulumuka. M’kupita kwa nthawi Nowa ndi banja lake anafa, koma Mulungu adzawaukitsa ndipo adzakhala ndi ciyembekezo ca moyo wamuyaya.

Mulungu adzaononganso anthu oipa ndi kupulumutsa abwino. Mateyu 24:37-39

Satana ndi viŵanda vake amaseŵenzetsa njila zambili pofuna kusoceletsa anthu

Satana ndi viŵanda vake akali kusokoneza anthu.

Masiku ano, monga m’nthawi ya Nowa, anthu ambili amakana malangizo acikondi a Yehova. Posacedwa Yehova adzaononga anthu onse oipa.—2 Petulo 2:5, 6.

Mboni za Yehova ziseŵenzetsa Baibo polalikila munthu; munthu aŵelenga Baibo

Anthu ena ali ngati Nowa. Iwo amamvetsela kwa Mulungu ndi kucita zimene iye amakamba; anthu amenewo ni Mboni za Yehova.

  • Sankhani njila yopita kumoyo.—Mateyu 7:13, 14.

  • Oipa adzaonongedwa; ofatsa adzasangalala ndi mtendele.—Salimo 37:10, 11.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani