-
Numeri 26:15-17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ana aamuna a Gadi+ potengera mabanja awo anali awa: Zefoni amene anali kholo la banja la Azefoni, Hagi amene anali kholo la banja la Ahagi, Suni amene anali kholo la banja la Asuni, 16 Ozini amene anali kholo la banja la Aozini, Eri amene anali kholo la banja la Aeri, 17 Arodi amene anali kholo la banja la Aarodi ndi Areli amene anali kholo la banja la Aareli.
-