Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yoswa 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yosefe anali mafuko awiri,+ la Manase ndi la Efuraimu.+ Alevi sanapatsidwe cholowa cha malo koma anangowapatsa mizinda+ yoti azikhalamo komanso malo odyetserako ziweto ndi osungirako katundu wawo.+

  • 1 Mbiri 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ana a Rubeni,+ mwana woyamba wa Isiraeli anali awa: Rubeni anali woyamba kubadwa koma chifukwa chakuti anaipitsa bedi la bambo ake,+ udindo wake monga woyamba kubadwa unaperekedwa kwa ana a Yosefe,+ mwana wa Isiraeli. Choncho iye sanalembedwe monga woyamba kubadwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani