-
Deuteronomo 33:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ponena za Nafitali anati:+
“Nafitali wakhutira chifukwa chovomerezedwa,
Ndipo madalitso a Yehova amuchulukira.
Tenga chigawo chakumadzulo ndi kumʼmwera.”
-