Genesis 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musalimbane nawo,* chifukwa sindikupatsani mbali iliyonse ya dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha, chifukwa ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+ Yoswa 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo Isaki ndinamʼpatsa Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinamʼpatsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+
5 Musalimbane nawo,* chifukwa sindikupatsani mbali iliyonse ya dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha, chifukwa ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+
4 ndipo Isaki ndinamʼpatsa Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinamʼpatsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+