Salimo 105:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu anachititsa kuti anthu ake aberekane kwambiri,+Iye anawachititsa kuti akhale amphamvu kwambiri kuposa adani awo.+25 Analola adaniwo kuti asinthe mitima yawo nʼkuyamba kudana ndi anthu ake,Komanso kukonzera chiwembu atumiki akewo.+
24 Mulungu anachititsa kuti anthu ake aberekane kwambiri,+Iye anawachititsa kuti akhale amphamvu kwambiri kuposa adani awo.+25 Analola adaniwo kuti asinthe mitima yawo nʼkuyamba kudana ndi anthu ake,Komanso kukonzera chiwembu atumiki akewo.+