Ekisodo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Ekisodo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anakuuzani pangano lake,+ kapena kuti Malamulo Khumi,*+ amene anakulamulani kuti muziwatsatira. Kenako analemba Malamulowo pamiyala iwiri yosema.+ Deuteronomo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako ndinatembenuka nʼkutsika mʼphirimo pa nthawi imene phirilo linkayaka moto,+ ndipo miyala iwiri ya pangano inali mʼmanja mwanga.+
13 Iye anakuuzani pangano lake,+ kapena kuti Malamulo Khumi,*+ amene anakulamulani kuti muziwatsatira. Kenako analemba Malamulowo pamiyala iwiri yosema.+
15 Kenako ndinatembenuka nʼkutsika mʼphirimo pa nthawi imene phirilo linkayaka moto,+ ndipo miyala iwiri ya pangano inali mʼmanja mwanga.+