Deuteronomo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nditayangʼana, ndinaona kuti mwachimwira Yehova Mulungu wanu. Munali mutadzipangira mwana wa ngʼombe wachitsulo.* Munali mutapatuka mofulumira panjira imene Yehova anakulamulani kuti muziyendamo.+ Yesaya 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali anthu amene amakhuthula golide mʼzikwama zawo.Amayeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kumuweramira ndi kumulambira.*+ Machitidwe 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
16 Nditayangʼana, ndinaona kuti mwachimwira Yehova Mulungu wanu. Munali mutadzipangira mwana wa ngʼombe wachitsulo.* Munali mutapatuka mofulumira panjira imene Yehova anakulamulani kuti muziyendamo.+
6 Pali anthu amene amakhuthula golide mʼzikwama zawo.Amayeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kumuweramira ndi kumulambira.*+