-
Nehemiya 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ngakhale pamene anapanga chifaniziro chachitsulo cha mwana wa ngʼombe nʼkuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu amene anakutulutsani ku Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,
-