-
Numeri 14:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiwagwetsera mliri ndi kuwawononga, ndipo iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kuposa iwowa.”+
-
-
Deuteronomo 9:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndisiye kuti ndiwawononge nʼkufafaniza dzina lawo pansi pa thambo, ndipo ndikupange iweyo kukhala mtundu wamphamvu komanso waukulu kwambiri kuposa iwowo.’+
-