Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 7:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nsembe iliyonse yambewu imene yaphikidwa mu uvuni kapena mʼchiwaya+ izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo. Izikhala yake.+ 10 Koma nsembe yambewu iliyonse yothira mafuta+ kapena yosathira mafuta+ izikhala ya ana onse aamuna a Aroni, azigawana mofanana.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani