-
Levitiko 6:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ndipo chiwiya chadothi chimene mungawiritsiremo nyamayo muzichiswa. Koma mukawiritsira mʼchiwiya chakopa,* muzichikwecha nʼkuchitsuka ndi madzi.
-