-
Levitiko 16:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Akatero azituluka nʼkupita kuguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova kuti akaliphimbire machimo. Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ngʼombe yamphongo ndi a mbuzi nʼkuwapaka panyanga zonse za guwa lansembe.
-