-
Levitiko 5:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako azidontheza ena mwa magazi a nsembe yamachimo mʼmbali mwa guwa lansembe, koma magazi otsalawo aziwathira pansi pa guwa lansembelo.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.
-