-
Levitiko 27:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 MʼChaka cha Ufulu mundawo udzabwezedwa kwa mwiniwake weniweni amene anaugulitsa.+
-
-
Numeri 36:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiye chaka cha Ufulu+ cha Aisiraeli chikadzafika, cholowa cha akaziwa chidzachotsedwa ku cholowa cha fuko la makolo athu, ndipo chidzawonjezedwa ku cholowa cha fuko limene aliyense wa iwo adzakwatiweko ndipo chidzakhala cha fukolo mpaka kalekale.”
-