-
Levitiko 27:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma ngati akupereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika mʼChaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake womwe unaikidwa.+
-