Deuteronomo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukawoloka Yorodano+ nʼkukakhala mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu, adzakutetezani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhala otetezeka.+ Salimo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzagona pansi mwamtendere nʼkupeza tulo,+Chifukwa inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+ Miyambo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma munthu wondimvera adzakhala motetezeka+Ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+
10 Mukawoloka Yorodano+ nʼkukakhala mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu, adzakutetezani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhala otetezeka.+
8 Ndidzagona pansi mwamtendere nʼkupeza tulo,+Chifukwa inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+