- 
	                        
            
            Numeri 35:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        4 Malo odyetserako ziweto a mizinda imene mukapereke kwa Aleviwo, akakhale mamita 445* kuchokera pampanda wa mzindawo kuzungulira mzinda wonse. 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Deuteronomo 18:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        18 “Alevi omwe ndi ansembe, komanso fuko lonse la Levi, sadzapatsidwa gawo kapena cholowa pakati pa Aisiraeli. Iwo azidzadya nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, zomwe ndi cholowa chake.+ 
 
-