-
Levitiko 25:55Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
55 Chifukwa Aisiraeli ndi akapolo anga. Iwo ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
-