-
Numeri 34:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho Mose anauza Aisiraeli kuti: “Limeneli ndi dziko limene ligawidwe kwa inu pogwiritsa ntchito maere kuti likhale cholowa chanu.+ Lidzagawidwa kwa inu mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kuti liperekedwe kwa mafuko 9 ndi hafu.
-