Levitiko 10:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mayina a ana a Aroni anali awa: woyamba Nadabu kenako Abihu,+ Eleazara+ ndi Itamara.+ Numeri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova atapereka moto wosaloledwa kwa Yehova+ mʼchipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Pomwe Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo. 1 Mbiri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nadabu ndi Abihu anamwalira opanda ana aamuna bambo awo adakali ndi moyo,+ koma Eliezara+ ndi Itamara ankatumikirabe ngati ansembe.
4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova atapereka moto wosaloledwa kwa Yehova+ mʼchipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Pomwe Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo.
2 Nadabu ndi Abihu anamwalira opanda ana aamuna bambo awo adakali ndi moyo,+ koma Eliezara+ ndi Itamara ankatumikirabe ngati ansembe.