-
Yoswa 17:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Tselofekadi+ mwana wa Heferi, mwana wa Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana aamuna, koma aakazi okhaokha. Mayina a anawo anali Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza. 4 Iwo anapita kwa wansembe Eliezara,+ Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri, nʼkuwauza kuti: “Yehova ndi amene analamula Mose kuti atipatse cholowa pakati pa abale athu.”+ Choncho anawapatsa cholowa pakati pa azichimwene a bambo awo, pomvera lamulo la Yehova.+
-