Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 20:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Numeri 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe nʼkuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika mʼphirimo.

  • Numeri 33:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Wansembe Aroni anakwera mʼphiri la Hora mogwirizana ndi zimene Yehova analamula, ndipo anamwalira mʼphirimo mʼchaka cha 40 mʼmwezi wa 5 pa tsiku loyamba la mweziwo kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo.+

  • Deuteronomo 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Deuteronomo 32:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani