Deuteronomo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yoswa mwana wa Nuni anali atadzazidwa ndi mzimu wa nzeru, chifukwa Mose anaika manja ake pa iye.+ Aisiraeli anayamba kumumvera ndipo anachita mogwirizana ndi zomwe Yehova analamula Mose.+ Machitidwe 6:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
9 Yoswa mwana wa Nuni anali atadzazidwa ndi mzimu wa nzeru, chifukwa Mose anaika manja ake pa iye.+ Aisiraeli anayamba kumumvera ndipo anachita mogwirizana ndi zomwe Yehova analamula Mose.+