Deuteronomo 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira+ ndi amene akalowe mʼdzikomo.+ Umulimbitse,*+ chifukwa ndi amene adzatsogolere Aisiraeli pokatenga dzikolo kukhala lawo.”) Deuteronomo 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova Mulungu wanu akuwoloka patsogolo panu kuti akutsogolereni. Iye adzawononga mitundu imeneyi pamaso panu ndipo inu mudzaithamangitsa.+ Yoswa ndi amene akutsogolereni nʼkukuwolotsani,+ mogwirizana ndi zimene Yehova wanena. Deuteronomo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mu Isiraeli simunakhalenso mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova ankamudziwa bwino kwambiri.*+
38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira+ ndi amene akalowe mʼdzikomo.+ Umulimbitse,*+ chifukwa ndi amene adzatsogolere Aisiraeli pokatenga dzikolo kukhala lawo.”)
3 Yehova Mulungu wanu akuwoloka patsogolo panu kuti akutsogolereni. Iye adzawononga mitundu imeneyi pamaso panu ndipo inu mudzaithamangitsa.+ Yoswa ndi amene akutsogolereni nʼkukuwolotsani,+ mogwirizana ndi zimene Yehova wanena.
10 Koma mu Isiraeli simunakhalenso mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova ankamudziwa bwino kwambiri.*+