- 
	                        
            
            Salimo 94:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+ Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu! 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Yesaya 1:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti: “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga, Ndipo ndidzabwezera adani anga.+ 
 
-