-
Levitiko 26:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mudzathamangitsa adani anu ndi kuwagonjetsa ndi lupanga. 8 Anthu anu 5 adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+
-